-
Numeri 17:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Tsiku lotsatira, Mose atalowa m’chihema cha Umbonicho, anangoona kuti ndodo ya Aroni ya nyumba ya Levi inali itaphuka. Ndodoyo inali itaphuka ndipo inali kumasula maluwa ndi kubala zipatso za amondi zakupsa.
-