Numeri 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo+ ya Aroni patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana a chipandukowa,+ n’cholinga chakuti aleke kudandaula motsutsana ndi ine, kuti angafe.”
10 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Bwezera ndodo+ ya Aroni patsogolo pa Umboni. Uisunge kuti ikhale chikumbutso+ kwa ana a chipandukowa,+ n’cholinga chakuti aleke kudandaula motsutsana ndi ine, kuti angafe.”