Numeri 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zipatso zonse zoyamba kupsa m’minda yawo, zimene azizipereka kwa Yehova zizikhala zako.+ Aliyense wa m’nyumba yako amene ndi wosadetsedwa azidya nawo.
13 Zipatso zonse zoyamba kupsa m’minda yawo, zimene azizipereka kwa Yehova zizikhala zako.+ Aliyense wa m’nyumba yako amene ndi wosadetsedwa azidya nawo.