Numeri 18:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwanayo uzimuwombola ndi dipo akakwanitsa mwezi umodzi kapena kuposerapo. Uzimuwombola ndi mtengo woikidwiratu, masekeli asiliva asanu, malinga ndi sekeli la kumalo oyera,+ lofanana ndi magera+ 20.
16 Mwanayo uzimuwombola ndi dipo akakwanitsa mwezi umodzi kapena kuposerapo. Uzimuwombola ndi mtengo woikidwiratu, masekeli asiliva asanu, malinga ndi sekeli la kumalo oyera,+ lofanana ndi magera+ 20.