Numeri 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kunena za ana a Levi, iwo ndawapatsa chakhumi+ chilichonse mu Isiraeli monga cholowa chawo chifukwa cha utumiki wawo umene akuchita, utumiki wa pachihema chokumanako. Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:21 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, article 170
21 “Kunena za ana a Levi, iwo ndawapatsa chakhumi+ chilichonse mu Isiraeli monga cholowa chawo chifukwa cha utumiki wawo umene akuchita, utumiki wa pachihema chokumanako.