Numeri 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aleviwo azichita utumiki wawo pachihema chokumanako, ndipo ndiwo amene azisenza zolakwa za anthuwo.+ Iwo asakhale ndi cholowa+ pakati pa ana a Isiraeli. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale m’mibadwo yanu yonse.
23 Aleviwo azichita utumiki wawo pachihema chokumanako, ndipo ndiwo amene azisenza zolakwa za anthuwo.+ Iwo asakhale ndi cholowa+ pakati pa ana a Isiraeli. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale m’mibadwo yanu yonse.