Numeri 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Lankhula ndi Alevi, uwauze kuti, ‘Muzilandira kwa ana a Isiraeli chakhumi chimene ndakupatsani monga cholowa+ chanu. Ndipo pachakhumi chimene muzilandiracho, muziperekapo chopereka chanu kwa Yehova, chakhumi cha chakhumicho.+
26 “Lankhula ndi Alevi, uwauze kuti, ‘Muzilandira kwa ana a Isiraeli chakhumi chimene ndakupatsani monga cholowa+ chanu. Ndipo pachakhumi chimene muzilandiracho, muziperekapo chopereka chanu kwa Yehova, chakhumi cha chakhumicho.+