Numeri 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Wansembeyo atenge mtengo wa mkungudza,+ kamtengo ka hisope+ ndi ulusi wofiira kwambiri,+ aziponye pakati pa moto umene akutenthapo ng’ombeyo.
6 Wansembeyo atenge mtengo wa mkungudza,+ kamtengo ka hisope+ ndi ulusi wofiira kwambiri,+ aziponye pakati pa moto umene akutenthapo ng’ombeyo.