Numeri 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Wowola phulusa la ng’ombeyo azichapa zovala zake, koma azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.+ “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+
10 Wowola phulusa la ng’ombeyo azichapa zovala zake, koma azikhalabe wodetsedwa mpaka madzulo.+ “‘Limeneli likhale lamulo mpaka kalekale kwa ana a Isiraeli ndi kwa mlendo wokhala pakati pawo.+