Numeri 19:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chinthu chilichonse chimene munthu wodetsedwayo angakhudze, chikhale chodetsedwa.+ Komanso munthu amene angakhudze chinthucho, akhale wodetsedwa mpaka madzulo.’”+
22 Chinthu chilichonse chimene munthu wodetsedwayo angakhudze, chikhale chodetsedwa.+ Komanso munthu amene angakhudze chinthucho, akhale wodetsedwa mpaka madzulo.’”+