Numeri 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo n’kupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+
6 Pamenepo Mose ndi Aroni anachoka pamaso pa mpingowo n’kupita kukhomo la chihema chokumanako. Kumeneko, anagwada n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi,+ ndipo ulemerero wa Yehova unayamba kuonekera kwa iwo.+