Numeri 20:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Choncho mfumu ya Edomu inakana kulola Aisiraeli kudzera m’dziko lake.+ Motero, Aisiraeli analambalala dziko la Edomu.+
21 Choncho mfumu ya Edomu inakana kulola Aisiraeli kudzera m’dziko lake.+ Motero, Aisiraeli analambalala dziko la Edomu.+