Numeri 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako khamu lonse la ana a Isiraeli linanyamuka ku Kadesi+ kuja n’kukafika kuphiri la Hora.+