Numeri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+
26 M’phirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ n’kuveka mwana wake Eleazara.+ Aroni akamwalira kumeneko n’kugona ndi makolo ake.”+