Numeri 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.
22 Kenako, ana a Isiraeli anasamuka kumaloko n’kukamanga msasa m’chipululu cha Mowabu,+ moyang’anana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.