Numeri 22:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo akalonga a ku Mowabu aja ananyamuka n’kubwerera kwa Balaki, ndipo anakamuuza kuti: “Balamu wakana kubwera nafe.”+
14 Pamenepo akalonga a ku Mowabu aja ananyamuka n’kubwerera kwa Balaki, ndipo anakamuuza kuti: “Balamu wakana kubwera nafe.”+