Numeri 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 M’mawa kutacha, Balamu anadzuka n’kumanga chishalo pabulu* wake, ndipo anapita limodzi ndi akalonga a ku Mowabu aja.+
21 M’mawa kutacha, Balamu anadzuka n’kumanga chishalo pabulu* wake, ndipo anapita limodzi ndi akalonga a ku Mowabu aja.+