Numeri 22:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Inetu sindingathe kunena kalikonse.+ Mawu amene Yehova ati aike m’kamwa mwangamu ndi amene ndilankhule.”+
38 Balamu anayankha Balaki kuti: “Si ine ndabwerane! Inetu sindingathe kunena kalikonse.+ Mawu amene Yehova ati aike m’kamwa mwangamu ndi amene ndilankhule.”+