Numeri 23:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Chotero Balaki anachita monga momwe Balamu ananenera. Anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
30 Chotero Balaki anachita monga momwe Balamu ananenera. Anapereka nsembe ng’ombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+