Numeri 24:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano Balamu ananyamuka kumabwerera kwawo.+ Nayenso Balaki ananyamuka kulowera njira yake.