Numeri 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+
13 Likhale pangano la unsembe kwa iye ndi mbadwa zake mpaka kalekale,+ chifukwa sanalekerere zoti anthu azipikisana ndi Mulungu wake,+ ndiponso waphimba machimo a ana a Isiraeli.’”+