Numeri 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Werengani amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, potsata nyumba za makolo awo.”+
2 “Werengani amuna onse oyenera kupita kunkhondo pakati pa khamu lonse la ana a Isiraeli. Muwerenge kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, potsata nyumba za makolo awo.”+