Numeri 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Werengani ana onse a Isiraeli kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, monga Yehova analamulira Mose.”+ Tsopano ana onse a Isiraeli amene anatuluka m’dziko la Iguputo ndi awa:
4 “Werengani ana onse a Isiraeli kuyambira azaka 20 kupita m’tsogolo, monga Yehova analamulira Mose.”+ Tsopano ana onse a Isiraeli amene anatuluka m’dziko la Iguputo ndi awa: