Numeri 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Rubeni anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli.+ Ana aamuna a Rubeni anali: Hanoki+ amene anali kholo la banja la Ahanoki, Palu+ amene anali kholo la banja la Apalu,
5 Rubeni anali mwana woyamba kubadwa wa Isiraeli.+ Ana aamuna a Rubeni anali: Hanoki+ amene anali kholo la banja la Ahanoki, Palu+ amene anali kholo la banja la Apalu,