Numeri 26:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani+ ndi Abiramu.+ Awiriwa, Datani ndi Abiramu, anali osankhidwa a khamulo. Iwowa ndi amene anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose ndi Aroni, pamene anali kutsutsana ndi Yehova.
9 Ana aamuna a Eliyabu anali Nemueli, Datani+ ndi Abiramu.+ Awiriwa, Datani ndi Abiramu, anali osankhidwa a khamulo. Iwowa ndi amene anagwirizana ndi gulu la Kora+ pokangana ndi Mose ndi Aroni, pamene anali kutsutsana ndi Yehova.