Numeri 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Amenewa ndiwo anali mabanja a Manase. Amuna onse owerengedwa m’mabanja awo analipo 52,700.+