Numeri 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu,
38 Ana aamuna a Benjamini+ ndi mabanja awo anali awa: Bela+ amene anali kholo la banja la Abela, Asibeli+ amene anali kholo la banja la Aasibeli, Ahiramu amene anali kholo la banja la Aahiramu,