Numeri 26:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ana aamuna a Dani+ mwa mabanja awo anali ochokera kwa Suhamu amene anali kholo la banja la Asuhamu. Awa anali mabanja a Dani+ potsata fuko lawo.
42 Ana aamuna a Dani+ mwa mabanja awo anali ochokera kwa Suhamu amene anali kholo la banja la Asuhamu. Awa anali mabanja a Dani+ potsata fuko lawo.