Numeri 26:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ana aamuna a Aseri+ ndi mabanja awo anali awa: Imuna+ amene anali kholo la banja la Aimuna, Isivi+ amene anali kholo la banja la Aisivi ndi Beriya amene anali kholo la banja la Aberiya.
44 Ana aamuna a Aseri+ ndi mabanja awo anali awa: Imuna+ amene anali kholo la banja la Aimuna, Isivi+ amene anali kholo la banja la Aisivi ndi Beriya amene anali kholo la banja la Aberiya.