Numeri 26:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ana aamuna a Beriya anali Hiberi amene anali kholo la banja la Ahiberi, ndi Malikieli+ amene anali kholo la banja la Amalikieli.
45 Ana aamuna a Beriya anali Hiberi amene anali kholo la banja la Ahiberi, ndi Malikieli+ amene anali kholo la banja la Amalikieli.