Numeri 26:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Iwowa sanawerengedwe limodzi ndi ana a Isiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa ana a Isiraeli.+
62 Onse amene anawerengedwa pakati pa Alevi analipo 23,000. Amenewa anali amuna onse kuyambira amwezi umodzi kupita m’tsogolo.+ Iwowa sanawerengedwe limodzi ndi ana a Isiraeli,+ chifukwa sanafunikire kulandira cholowa pakati pa ana a Isiraeli.+