Numeri 27:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mose anachitadi monga mmene Yehova anamulamulira. Anatenga Yoswa n’kumuimiritsa pamaso pa wansembe Eleazara,+ ndi pamaso pa khamu lonselo.
22 Mose anachitadi monga mmene Yehova anamulamulira. Anatenga Yoswa n’kumuimiritsa pamaso pa wansembe Eleazara,+ ndi pamaso pa khamu lonselo.