Numeri 27:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako anaika manja ake pa iye n’kumuika kukhala mtsogoleri+ monga Yehova ananenera kudzera kwa Moseyo.+
23 Kenako anaika manja ake pa iye n’kumuika kukhala mtsogoleri+ monga Yehova ananenera kudzera kwa Moseyo.+