Numeri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+
29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+ Lizikhala tsiku lanu loliza lipenga.+