Numeri 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi wamphongo, monga nsembe yamachimo yophimbira machimo anu.+