Numeri 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yambewu ndiponso nsembe yake yachakumwa.+
16 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo, kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yambewu ndiponso nsembe yake yachakumwa.+