Numeri 29:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo.+ Muzim’pereka kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu, limodzi ndi nsembe zake zachakumwa.+
19 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo.+ Muzim’pereka kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku ndi nsembe yake yambewu, limodzi ndi nsembe zake zachakumwa.+