Numeri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “‘Pa tsiku lachitatu, muzipereka ng’ombe 11 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
20 “‘Pa tsiku lachitatu, muzipereka ng’ombe 11 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+