Numeri 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe zamphongo, nkhosa zamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.
21 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe zamphongo, nkhosa zamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.