Numeri 29:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo,+ kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku,+ limodzi ndi nsembe yake yambewu, ndiponso nsembe yake yachakumwa.+
25 Muziperekanso mwana wa mbuzi mmodzi monga nsembe yamachimo,+ kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku,+ limodzi ndi nsembe yake yambewu, ndiponso nsembe yake yachakumwa.+