Numeri 29:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Pa tsiku lachisanu, muzipereka ng’ombe 9 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
26 “‘Pa tsiku lachisanu, muzipereka ng’ombe 9 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+