Numeri 29:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku la 6, muzipereka ng’ombe 8 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+
29 “‘Pa tsiku la 6, muzipereka ng’ombe 8 zamphongo, nkhosa ziwiri zamphongo, ndi ana a nkhosa 14 amphongo, ndipo mwana wa nkhosa aliyense azikhala wachaka chimodzi, wopanda chilema.+