Numeri 29:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Muziperekanso mbuzi imodzi monga nsembe yamachimo,+ kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yambewu, ndiponso nsembe yake yachakumwa.+
34 Muziperekanso mbuzi imodzi monga nsembe yamachimo,+ kuwonjezera pa nsembe yopsereza ya tsiku ndi tsiku, limodzi ndi nsembe yake yambewu, ndiponso nsembe yake yachakumwa.+