Numeri 29:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “‘Pa tsiku la 8, muzichita msonkhano wapadera.+ Musamagwire ntchito yolemetsa yamtundu uliwonse.+