Numeri 29:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe yamphongo, nkhosa yamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.+
37 Popereka nyama zimenezi, ng’ombe yamphongo, nkhosa yamphongo, ndi ana a nkhosa amphongo, muziperekanso nsembe zake zambewu+ ndi nsembe zake zachakumwa,+ malinga ndi kuchuluka kwa nyamazo, potsatira dongosolo la nthawi zonse.+