Numeri 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose analankhula ndi anthuwo, kuti: “Konzekeretsani amuna pakati panu, apite kunkhondo. Apite kukamenyana ndi Amidiyani, kuti Yehova awalange Amidiyaniwo pobwezera zimene anachita.+
3 Chotero Mose analankhula ndi anthuwo, kuti: “Konzekeretsani amuna pakati panu, apite kunkhondo. Apite kukamenyana ndi Amidiyani, kuti Yehova awalange Amidiyaniwo pobwezera zimene anachita.+