Numeri 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mizinda yawo yonse imene anali kukhalamo, ndi misasa yawo yonse ya mipanda anaitentha ndi moto.+