Numeri 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anatenga zonse zimene anafunkha,+ zomwe zinaphatikizapo anthu ndi ziweto zomwe.