Numeri 31:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chilichonse chimene sichingapse ndi moto,+ chidutse pamoto kuti chikhale choyera. Muchiyeretsenso ndi madzi.+ Koma chilichonse chimene chingapse ndi moto muchiyeretse ndi madzi.+
23 chilichonse chimene sichingapse ndi moto,+ chidutse pamoto kuti chikhale choyera. Muchiyeretsenso ndi madzi.+ Koma chilichonse chimene chingapse ndi moto muchiyeretse ndi madzi.+