Numeri 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Zimenezi muzitenge pa hafu imene iwo ati alandire, ndipo muzipereke kwa wansembe Eleazara monga chopereka kwa Yehova.+
29 Zimenezi muzitenge pa hafu imene iwo ati alandire, ndipo muzipereke kwa wansembe Eleazara monga chopereka kwa Yehova.+